Mateyu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anatembenuka ndipo anaona mayiyo nʼkunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+ Luka 8:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Mwanawe, chikhulupiriro chako chakuchiritsa. Pita mu mtendere.”+
22 Yesu anatembenuka ndipo anaona mayiyo nʼkunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+