Genesis 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Ndidzabweranso kwa iwe pa nthawi ngati yomwe ino chaka chamawa, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.” Mateyu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+
14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Ndidzabweranso kwa iwe pa nthawi ngati yomwe ino chaka chamawa, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”
26 Yesu anawayangʼanitsitsa nʼkuwauza kuti: “Kwa anthu zimenezi nʼzosatheka, koma zinthu zonse nʼzotheka kwa Mulungu.”+