Mateyu 7:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pitirizani kupempha ndipo adzakupatsani.+ Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+ 8 Chifukwa aliyense wopempha amalandira,+ aliyense wofunafuna amapeza, ndipo aliyense wogogoda adzamutsegulira.
7 Pitirizani kupempha ndipo adzakupatsani.+ Pitirizani kufunafuna ndipo mudzapeza. Pitirizani kugogoda ndipo adzakutsegulirani.+ 8 Chifukwa aliyense wopempha amalandira,+ aliyense wofunafuna amapeza, ndipo aliyense wogogoda adzamutsegulira.