Ekisodo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga aja anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.
19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga aja anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanawamvere, mogwirizana ndi zimene Yehova ananena.