Chivumbulutso 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu nʼkuuponya mʼnyanja, ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+ Chivumbulutso 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwa iye munapezeka magazi a aneneri, a oyera,+ ndi a onse amene anaphedwa padziko lapansi.”+
21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu nʼkuuponya mʼnyanja, ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+