Luka 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, nʼcholinga choti akamupezere zifukwa pa zimene angalankhule,+ kuti akamupereke kuboma ndi kwa bwanamkubwa.
20 Ndiyeno ataonetsetsa zochita zake, anatuma aganyu mwachinsinsi kuti akadzionetse ngati olungama, nʼcholinga choti akamupezere zifukwa pa zimene angalankhule,+ kuti akamupereke kuboma ndi kwa bwanamkubwa.