Mateyu 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yesu atabadwa ku Betelehemu+ wa ku Yudeya, pa nthawi ya ulamuliro wa Mfumu Herode,*+ okhulupirira nyenyezi ochokera Kumʼmawa anabwera ku Yerusalemu.
2 Yesu atabadwa ku Betelehemu+ wa ku Yudeya, pa nthawi ya ulamuliro wa Mfumu Herode,*+ okhulupirira nyenyezi ochokera Kumʼmawa anabwera ku Yerusalemu.