-
1 Mafumu 1:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Komanso mfumu inanena kuti, ‘Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ndipo walola kuti maso anga aone zimenezi.’”
-
-
Salimo 106:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndipo anthu onse anene kuti, “Ame!”
Tamandani Ya,*
-