Maliko 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho khalanibe maso chifukwa simukudziwa nthawi imene mwininyumba adzabwere.+ Simukudziwa ngati adzabwere madzulo, pakati pa usiku, mʼmbandakucha* kapena mʼmamawa,+
35 Choncho khalanibe maso chifukwa simukudziwa nthawi imene mwininyumba adzabwere.+ Simukudziwa ngati adzabwere madzulo, pakati pa usiku, mʼmbandakucha* kapena mʼmamawa,+