-
Mateyu 16:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma Yesu anawayankha kuti: “Kunja kukamada mumanena kuti, ‘Nyengo ikhala yabwino, chifukwa kumwamba kwafiira ngati moto.’ 3 Koma mʼmawa mumanena kuti, ‘Lero kukuoneka kuti kugwa mvula, chifukwa kumwamba kwafiira ndipo kuli mitambo.’ Mumadziwa kumasulira kaonekedwe ka kumwamba, koma mukulephera kumasulira zizindikiro za nthawi ino.
-