-
Mateyu 5:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Uzithetsa nkhani mofulumira ndi munthu wokuimba mlandu pamene ukupita naye kukhoti, kuti mwina wokuimba mlanduyo asakakupereke kwa woweruza. Komanso kuti woweruzayo asakakupereke kwa msilikali wakukhoti kuti akuponye mʼndende.+ 26 Kunena zoona, sudzatulukamo mpaka utalipira kakhobidi kotsirizira kochepa mphamvu kwambiri.*
-