Levitiko 11:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake nʼzogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ndi yodetsedwa kwa inu. 8 Musamadye nyama iliyonse ya zimenezi, ndipo nyamazi zikafa musamazikhudze. Ndi zodetsedwa kwa inu.+
7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake nʼzogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ndi yodetsedwa kwa inu. 8 Musamadye nyama iliyonse ya zimenezi, ndipo nyamazi zikafa musamazikhudze. Ndi zodetsedwa kwa inu.+