Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndipo musapereke matupi* anu ku uchimo kuti akhale zida zochitira zinthu zosalungama, koma dziperekeni kwa Mulungu ngati anthu amene aukitsidwa. Matupi anunso muwapereke kwa Mulungu ngati zida zochitira chilungamo.+

  • Aefeso 2:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma popeza kuti Mulungu ndi wachifundo chochuluka,+ komanso chifukwa cha chikondi chake chachikulu chimene anatisonyeza,+ 5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena