1 Mbiri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide, komanso Zadoki+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo mʼmagulu mogwirizana ndi udindo wa utumiki wawo. 1 Mbiri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 a 7 Hakozi, a 8 Abiya,+
3 Davide, komanso Zadoki+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo mʼmagulu mogwirizana ndi udindo wa utumiki wawo.