1 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma monga ana ongobadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasungunula* umene uli mʼMawu a Mulungu. Mukamamwa mkaka umenewo, ukuthandizani kuti mukule nʼkukhala oyenera chipulumutso.+
2 Koma monga ana ongobadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasungunula* umene uli mʼMawu a Mulungu. Mukamamwa mkaka umenewo, ukuthandizani kuti mukule nʼkukhala oyenera chipulumutso.+