-
Luka 5:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno anthu onsewo anadabwa kwambiri ndipo anayamba kutamanda Mulungu, moti anagwidwa ndi mantha. Iwo ankanena kuti: “Komatu lero ndiye taona zodabwitsa!”
-