Danieli 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtsinje wa moto unkayenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana 1 miliyoni* amene ankatumikira nthawi zonse ndi atumiki enanso 100 miliyoni* amene ankatumikira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linayamba kuzenga mlandu ndipo mabuku anatsegulidwa. Chivumbulutso 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, ndinaona ndi kumva mawu a angelo ambiri atazungulira mpando wachifumu limodzi ndi angelo 4 komanso akulu aja. Chiwerengero chawo chinali 10 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande* ndiponso mamiliyoni kuchulukitsa ndi masauzande.+
10 Mtsinje wa moto unkayenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana 1 miliyoni* amene ankatumikira nthawi zonse ndi atumiki enanso 100 miliyoni* amene ankatumikira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linayamba kuzenga mlandu ndipo mabuku anatsegulidwa.
11 Kenako, ndinaona ndi kumva mawu a angelo ambiri atazungulira mpando wachifumu limodzi ndi angelo 4 komanso akulu aja. Chiwerengero chawo chinali 10 sauzande kuchulukitsa ndi 10 sauzande* ndiponso mamiliyoni kuchulukitsa ndi masauzande.+