Luka 19:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda wazisonga kukuzungulira. Adaniwo adzakutsekereza nʼkukuukira* kuchokera kumbali zonse.+
43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda wazisonga kukuzungulira. Adaniwo adzakutsekereza nʼkukuukira* kuchokera kumbali zonse.+