-
1 Atesalonika 5:2, 3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Chifukwa inuyo mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati wakuba usiku.+ 3 Akadzangonena kuti, “Bata ndi mtendere!” nthawi yomweyo adzawonongedwa. Tsoka limeneli lidzawagwera modzidzimutsa+ ngati ululu umene mkazi woyembekezera amamva akatsala pangʼono kubereka ndipo sadzapulumuka.
-