Yeremiya 31:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso nyumba ya Yuda,” akutero Yehova.+ Aheberi 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mogwirizana ndi zimenezi, Yesu wakhala chikole cha pangano labwino kwambiri.+ Aheberi 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa Mulungu akuona kuti anthu akulakwitsa zinazake choncho iye akunena kuti: “‘Taonani! Masiku akubwera pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ akutero Yehova.*
31 “Taonani! Masiku akubwera, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso nyumba ya Yuda,” akutero Yehova.+
8 Chifukwa Mulungu akuona kuti anthu akulakwitsa zinazake choncho iye akunena kuti: “‘Taonani! Masiku akubwera pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ akutero Yehova.*