Mateyu 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithudi ndikukuuza iwe, usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+ Maliko 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero Yesu anamuyankha kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe kuti lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+ Luka 22:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Zitatero Ambuye anacheuka nʼkuyangʼana Petulo, ndipo Petulo anakumbukira mawu amene Ambuye anamuuza aja akuti: “Tambala asanalire lero, undikana katatu.”+ Yohane 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, tambala asanalire undikana katatu.”+
34 Yesu anamuuza kuti: “Ndithudi ndikukuuza iwe, usiku womwe uno tambala asanalire, undikana katatu.”+
30 Atatero Yesu anamuyankha kuti: “Ndithu ndikukuuza iwe kuti lero, usiku womwe uno, tambala asanalire kawiri, undikana katatu.”+
61 Zitatero Ambuye anacheuka nʼkuyangʼana Petulo, ndipo Petulo anakumbukira mawu amene Ambuye anamuuza aja akuti: “Tambala asanalire lero, undikana katatu.”+
38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, tambala asanalire undikana katatu.”+