Mateyu 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Khalani maso+ ndipo mupitirize kupemphera+ kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Maliko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Khalani maso ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Luka 22:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Iye anawauza kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukugona? Dzukani ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+
41 Khalani maso+ ndipo mupitirize kupemphera+ kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
38 Khalani maso ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
46 Iye anawauza kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukugona? Dzukani ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+