-
Yohane 19:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yesu anamuyankha kuti: “Simukanakhala ndi mphamvu iliyonse pa ine mukanapanda kupatsidwa kuchokera kumwamba. Nʼchifukwa chake munthu amene wandipereka kwa inu ali ndi tchimo lalikulu kwambiri.”
-