Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 50:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Msana wanga ndinaupereka kwa anthu amene ankandimenya

      Ndipo masaya anga ndinawapereka kwa anthu amene ankandizula ndevu.

      Sindinabise nkhope yanga kuti asaichitire zinthu zochititsa manyazi komanso kuti asailavulire.+

  • Yesaya 53:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+

      Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+

      Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+

      Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+

  • Mateyu 26:67, 68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 67 Ndiyeno anayamba kumulavulira kunkhope+ komanso kumumenya nkhonya.+ Ena anamuwomba mbama+ 68 nʼkunena kuti: “Losera tione Khristu iwe. Wakumenya ndi ndani?”

  • Maliko 14:65
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 65 Ndipo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope nʼkumamukhoma nkhonya. Iwo ankamuuza kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali apakhoti anamutenga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena