Salimo 69:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma mʼmalo mwa chakudya anandipatsa poizoni,*+Ndipo pamene ndinali ndi ludzu anandipatsa vinyo wosasa kuti ndimwe.+
21 Koma mʼmalo mwa chakudya anandipatsa poizoni,*+Ndipo pamene ndinali ndi ludzu anandipatsa vinyo wosasa kuti ndimwe.+