Yesaya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye adzakhala ngati malo opatulika,Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli,Adzakhala ngati mwala wopunthwitsa+Ndiponso ngati thanthwe lokhumudwitsa.Adzakhala ngati msampha komanso khwekhweKwa anthu okhala mu Yerusalemu.
14 Iye adzakhala ngati malo opatulika,Koma kwa nyumba zonse ziwiri za Isiraeli,Adzakhala ngati mwala wopunthwitsa+Ndiponso ngati thanthwe lokhumudwitsa.Adzakhala ngati msampha komanso khwekhweKwa anthu okhala mu Yerusalemu.