-
1 Petulo 2:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho iye ndi wamtengo wapatali kwa inu chifukwa mumamukhulupirira. Koma kwa amene samukhulupirira, “mwala umene omanga nyumba anaukana,+ wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.”+ 8 Wakhalanso “mwala wopunthwitsa ndi thanthwe lokhumudwitsa.”+ Anthu amenewa akupunthwa chifukwa samvera mawu, ndipo zimenezi nʼzimene zikuyenera kuwachitikira.
-