1 Akorinto 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa zinthu zoyambirira zimene ndinakuphunzitsani, zomwenso ineyo ndinalandira, panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, mogwirizana ndi Malemba.+ 1 Akorinto 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso zoti anaonekera kwa Kefa,*+ kenako kwa atumwi 12 aja.+
3 Pa zinthu zoyambirira zimene ndinakuphunzitsani, zomwenso ineyo ndinalandira, panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, mogwirizana ndi Malemba.+