Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+

  • Deuteronomo 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu+ mogwirizana ndi zimene Yehova Mulungu wanu anakulamulani, kuti mukhale ndi moyo nthawi yaitali komanso kuti zinthu zikuyendereni bwino mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+

  • Aefeso 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ana inu, muzimvera makolo anu+ mogwirizana ndi zimene Ambuye amafuna, chifukwa kuchita zimenezi nʼkoyenera.

  • Akolose 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ana inu, muzimvera makolo anu pa zinthu zonse,+ chifukwa zimenezi zimasangalatsa Ambuye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena