Akolose 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye ndi chifaniziro cha Mulungu wosaonekayo,+ woyamba kubadwa wa chilengedwe chonse.+ Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+ Chivumbulutso 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anavala malaya akunja amene anadonthera* magazi, ndipo amadziwika ndi dzina lakuti Mawu+ a Mulungu.
11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+
13 Iye anavala malaya akunja amene anadonthera* magazi, ndipo amadziwika ndi dzina lakuti Mawu+ a Mulungu.