Agalatiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipotu nonsenu ndinu ana a Mulungu+ chifukwa mumakhulupirira Khristu Yesu.+