Mateyu 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako mwamsanga, Yesu anauza ophunzira ake kuti akwere ngalawa nʼkutsogola kupita kutsidya lina. Koma iye anatsalira nʼcholinga choti auze anthuwo kuti azipita kwawo.+
22 Kenako mwamsanga, Yesu anauza ophunzira ake kuti akwere ngalawa nʼkutsogola kupita kutsidya lina. Koma iye anatsalira nʼcholinga choti auze anthuwo kuti azipita kwawo.+