Yohane 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mofanana ndi Atate amene ali ndi mphamvu zopereka moyo,*+ alolanso Mwana kuti akhale ndi mphamvu zopereka moyo.+ 1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Monga zilili kuti anthu onse amafa chifukwa cha Adamu,+ anthu onse adzapatsidwanso moyo kudzera mwa Khristu.+
26 Mofanana ndi Atate amene ali ndi mphamvu zopereka moyo,*+ alolanso Mwana kuti akhale ndi mphamvu zopereka moyo.+
22 Monga zilili kuti anthu onse amafa chifukwa cha Adamu,+ anthu onse adzapatsidwanso moyo kudzera mwa Khristu.+