Mateyu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼmasiku amenewo, Yohane+ Mʼbatizi anapita mʼchipululu cha Yudeya nʼkuyamba kulalikira.+ Mateyu 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye ankawabatiza* mumtsinje wa Yorodano+ ndipo anthuwo ankaulula machimo awo poyera.