Yohane 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno akuphunzitsa mʼkachisimo Yesu anafuula kuti: “Inu mukundidziwa komanso mukudziwa kumene ndikuchokera. Ine sindinabwere mwa kufuna kwanga,+ koma amene anandituma alipodi ndipo inu simukumudziwa.+
28 Ndiyeno akuphunzitsa mʼkachisimo Yesu anafuula kuti: “Inu mukundidziwa komanso mukudziwa kumene ndikuchokera. Ine sindinabwere mwa kufuna kwanga,+ koma amene anandituma alipodi ndipo inu simukumudziwa.+