Yohane 5:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, chifukwa ntchito zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ndikuchitazi, zikuchitira umboni kuti Atate ananditumadi.+
36 Koma ine ndili ndi umboni woposa wa Yohane, chifukwa ntchito zimene Atate wanga anandipatsa kuti ndizikwaniritse, ntchito zimene ndikuchitazi, zikuchitira umboni kuti Atate ananditumadi.+