Yohane 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 12 Kenako Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala kwa dziko.+ Aliyense wonditsatira ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala ndi kuwala+ kwa moyo.”
8 12 Kenako Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala kwa dziko.+ Aliyense wonditsatira ine sadzayenda mumdima, koma adzakhala ndi kuwala+ kwa moyo.”