-
Luka 10:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Koma Marita anatanganidwa ndi ntchito zambiri. Choncho anafika kwa Yesu nʼkunena kuti: “Ambuye, kodi sizikukukhudzani kuti mchemwali wangayu wandisiyira ndekha ntchito? Tamuuzeni kuti abwere adzandithandize.”
-