Yohane 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiye ndikapita kukakukonzerani malowo, ndidzabweranso kudzakutengerani kwathu, kuti kumene ine ndikakhale inunso mukakhale komweko.+ Yohane 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko a dziko.+ 1 Atesalonika 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pambuyo pake ife amene tidzakhale tidakali ndi moyo, limodzi ndi iwowo, tidzatengedwa kupita mʼmitambo+ kukakumana ndi Ambuye+ mumlengalenga ndipo tizikakhala ndi Ambuye nthawi zonse.+
3 Ndiye ndikapita kukakukonzerani malowo, ndidzabweranso kudzakutengerani kwathu, kuti kumene ine ndikakhale inunso mukakhale komweko.+
24 Atate, ine ndikufuna kuti amene mwandipatsawa adzakhale limodzi ndi ine kumene ine ndidzakhale,+ kuti adzaone ulemerero wanga umene inu mwandipatsa, chifukwa munandikonda musanayale maziko a dziko.+
17 Pambuyo pake ife amene tidzakhale tidakali ndi moyo, limodzi ndi iwowo, tidzatengedwa kupita mʼmitambo+ kukakumana ndi Ambuye+ mumlengalenga ndipo tizikakhala ndi Ambuye nthawi zonse.+