Aroma 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale zili choncho, si onse amene anatsatira uthenga wabwino. Chifukwa Yesaya anati: “Yehova,* kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+
16 Ngakhale zili choncho, si onse amene anatsatira uthenga wabwino. Chifukwa Yesaya anati: “Yehova,* kodi ndani wakhulupirira zimene anamva kwa ife?”+