Yohane 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndinabwera padzikoli ngati nthumwi yochokera kwa Atate. Tsopano ndikuchoka mʼdzikoli ndipo ndikupita kwa Atate.”+ Yohane 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine sindipitiriza kukhala mʼdzikoli chifukwa ndikubwera kwa inu, koma iwowo adakali mʼdzikoli.+ Atate Woyera, ayangʼanireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi* ngati mmene ife tilili.+
28 Ndinabwera padzikoli ngati nthumwi yochokera kwa Atate. Tsopano ndikuchoka mʼdzikoli ndipo ndikupita kwa Atate.”+
11 Ine sindipitiriza kukhala mʼdzikoli chifukwa ndikubwera kwa inu, koma iwowo adakali mʼdzikoli.+ Atate Woyera, ayangʼanireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi* ngati mmene ife tilili.+