Salimo 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngakhale munthu amene ndinkakhala naye mwamtendere, amene ndinkamukhulupirira,+Munthu amene ankadya chakudya changa, watukula chidendene chake nʼkundiukira.+ Mateyu 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anayankha kuti: “Amene akusunsa nane limodzi mʼmbalemu ndi amene andipereke.+
9 Ngakhale munthu amene ndinkakhala naye mwamtendere, amene ndinkamukhulupirira,+Munthu amene ankadya chakudya changa, watukula chidendene chake nʼkundiukira.+