Yohane 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mudzandifunafuna koma simudzandipeza, ndipo kumene ndidzapiteko inu simudzatha kukafikako.”+ Yohane 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho iye anawauzanso kuti: “Ine ndikuchoka ndipo mudzandifunafuna, koma mudzafa mudakali ochimwa.+ Kumene ine ndikupita inu simungathe kupitako.”+
21 Choncho iye anawauzanso kuti: “Ine ndikuchoka ndipo mudzandifunafuna, koma mudzafa mudakali ochimwa.+ Kumene ine ndikupita inu simungathe kupitako.”+