Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 13:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+

  • Yohane 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mukamasunga malamulo anga mudzachititsa kuti nthawi zonse ndizikukondani, mofanana ndi ine amene ndimasunga malamulo a Atate nʼkuchititsa kuti nthawi zonse azindikonda.

  • Yakobo 1:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena