Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 24:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndipo ine ndidzakutumizirani chimene Atate wanga anakulonjezani. Koma inu mukhalebe mumzindawu mpaka mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+

  • Yohane 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Akadzafika mthandizi amene ndidzakutumizireni kuchokera kwa Atate, amene ndi mzimu wa choonadi+ wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+

  • Yohane 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu.

  • Machitidwe 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chifukwa Yohane ankabatiza ndi madzi, koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera+ pasanathe masiku ambiri.”

  • Machitidwe 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano onse anali atasonkhana pamodzi pa tsiku la Chikondwerero cha Pentekosite.+

  • Machitidwe 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno onsewo anadzazidwa ndi mzimu woyera+ ndipo anayamba kulankhula zilankhulo zosiyanasiyana,* mogwirizana ndi mmene mzimuwo unawachititsira kulankhula.+

  • Aroma 8:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu umatithandiza pa zimene tikulephera kuchita.+ Chifukwa vuto ndi lakuti sitidziwa zimene tikufunika kutchula popemphera, koma mzimu umachonderera mʼmalo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena