Yohane 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yesu anawayankha kuti: “Nthawi yakuti Mwana wa munthu alemekezedwe yafika.+ Yohane 13:31, 32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yudasi atatuluka, Yesu anati: “Tsopano Mwana wa munthu walemekezedwa,+ ndipo Mulungu walemekezedwa kudzera mwa iye. 32 Mulungu amulemekeza+ ndipo amulemekeza nthawi yomwe ino.
31 Yudasi atatuluka, Yesu anati: “Tsopano Mwana wa munthu walemekezedwa,+ ndipo Mulungu walemekezedwa kudzera mwa iye. 32 Mulungu amulemekeza+ ndipo amulemekeza nthawi yomwe ino.