1 Yohane 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe, tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera padzikoli+ ndipo anatipatsa nzeru kuti tidziwe Mulungu woona. Kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu, ndife ogwirizana naye.+ Iyeyo ndi Mulungu woona ndipo amapereka moyo wosatha.+
20 Komabe, tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera padzikoli+ ndipo anatipatsa nzeru kuti tidziwe Mulungu woona. Kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu, ndife ogwirizana naye.+ Iyeyo ndi Mulungu woona ndipo amapereka moyo wosatha.+