-
Yohane 16:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Tadziwa tsopano kuti inu mukudziwa zinthu zonse ndipo mʼposafunikanso kuti munthu akufunseni mafunso. Pa chifukwa chimenechi tikukhulupirira kuti munachokeradi kwa Mulungu.”
-