Yohane 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mofanana ndi Atate amene amandikonda,+ inenso ndimakukondani. Choncho pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse kuti ndizikukondanibe.
9 Mofanana ndi Atate amene amandikonda,+ inenso ndimakukondani. Choncho pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse kuti ndizikukondanibe.