Mateyu 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda?” Yesu anayankha kuti: “Zili choncho, monga mmene mwanenera.”+ Yohane 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anatenga nthambi za kanjedza nʼkutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti: “Mʼpulumutseni! Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova,*+ amene ndi Mfumu ya Isiraeli!”+
11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda?” Yesu anayankha kuti: “Zili choncho, monga mmene mwanenera.”+
13 Choncho anatenga nthambi za kanjedza nʼkutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti: “Mʼpulumutseni! Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova,*+ amene ndi Mfumu ya Isiraeli!”+